...
MWAZIZIWA? > NKHANI > KODI NAMADINGO AKUFUNA KUMUONESA CHAKWERA NGATI OLEPHELA? WAONJEZA

KODI NAMADINGO AKUFUNA KUMUONESA CHAKWERA NGATI OLEPHELA? WAONJEZA

NAMADINGO VS CHAKWERA

Nde mwaimva? Patience Namadingo wati ndiwodabwa kwambiri ndi thandizo lomwe amalandira pa ntchito yomanga nyumba zophunzirira pasukulu ya pulaimale ya Watika ku Machinga.

Namadingo adanena izi pa 26 May 2025 atalandira ndalama zokwana K2.8 Million kuchokera kwa mmalawi okhalira ku dziko la United Kingdom, a Rodrick Chilumpha.

Iye wati ndi wokondwa kuti Amalawi ena akubwera kudzathandiza ntchitoyo, ponena kuti ndalamazi zithandiza kuchepetsa ndalama zomwe amawononga pa bajeti yake yoyamba.

Oimira a Rodrick Chilumpha, Thokozani Nkombezi wati dziko la Malawi likufunika ana enieni a nthaka ngati a Namadingo telo apempha ena kuti atengere khalidweli.

Nkombezi anawonjezera kuti, “Namadingo wasonyeza chifundo chake poonetsetsa kuti ophunzira akukhala mwamtendere chifukwa ambiri amaphunzirira pansi pa mitengo”. Mphunzitsi wamkulu pasukulu ya pulaimale ya Wataka, Stephano Nkhungwa, adati ntchitoyi idafika nthawi yake ndipo ophunzira adzapeza malo abwino ophunzirira akamaliza.

Koma ngakhale Namadingo akufuna school zipite pasogolo chonchi, nkhawa ilipobe pemene naye Trump wabwelesa nkhani yokudza pa maphunzilo athu pa dziko lonse kuphatikizapo Malawi, taimveni nkhani ya Trump iyi….


Celebrated music icon Patience Namadingo continues to capture the hearts of Malawians, not just through his music, but through meaningful action. On 26 May 2025, he expressed overwhelming gratitude for the growing support toward his initiative to construct a classroom block at Watika Primary School in Machinga. The latest boost came in the form of a generous K2.8 million donation from UK-based Malawian Rodrick Chilumpha, a contribution that significantly reduces the project’s overall costs. Namadingo praised the gesture, highlighting how collective effort can create lasting change in local communities.

But as the artist leads this noble cause, one must ask: why is it that musicians and private citizens are stepping in to do what politicians have consistently failed to prioritize? Rodrick Chilumpha’s representative, Thokozani Nkombezi, put it bluntly—Malawi needs more “true sons of the soil” like Namadingo. He emphasized that the artist’s compassion for learners, many of whom are forced to learn under trees, is what genuine leadership looks like. In contrast, elected officials continue to campaign with promises of improved education infrastructure, yet progress remains painfully slow or nonexistent in rural areas like Machinga.

The headteacher of Watika Primary School, Stephano Nkhungwa, called the project a timely intervention that will offer learners a safer, more conducive environment. But the situation raises a deeper issue: how many more children across Malawi are still studying in the open, waiting on promises that never materialize? Namadingo’s actions serve as both inspiration and indictment—a call for the nation to reevaluate its priorities and question why it takes artists, not policymakers, to build classrooms in 2025.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Seraphinite AcceleratorOptimized by Seraphinite Accelerator
Turns on site high speed to be attractive for people and search engines.