
KUGULISA MWANA NGATI MBUZI PA MTENGO WA K2,000,000
Eeeh koma KUTI mumve inuyo izi mmmh! Zimene zachitika ku South Africa zili ngati nthano komanso maloto. Akuti Mayi wina dzina lake Racquel “Kelly” Smith wachita zachilendo kwambiri, mpaka ma Judge owelura sanakhulupirire izi atamva. Mai uyu anagulitsa mwana wake wa zaka 6, dzina lake Joshlin, ngati akugulitsa nsima pamsika! Ndipo kuyimvetsetsa bwino nkhaniyi, akuti…