
BAE KUGULA ICHI MUKANILE CHIMUPHE YEKHA IWE MOYO WAKO UKHALEBE
Osazanena kuti ochenjeza panalibe. Mumve izi, akuti kafukufuku ku Canada wapeza umboni wamphamvu wosonyeza kuti kudya zakudya zambiri zokonzedwanso kwambiri kapena kuti over processed, monga zokhwasula-khwasula, zakudya zozizira, ndi chakudya cham’mawa maka zotsekemela za mgulu la ma cereals – kungayambitse matenda aakulu. Zakudya izi zili paliponse chifukwa ndizosavuta, zokoma, komanso zogulitsidwa kwambiri. Koma ofufuza akuti…