Waziziwa

MWAZIZIWA? > Articles by: Waziziwa
CHIMWENDO BANDA

KOMA CHIMWENDO AZASIYA BOZA LAKE LIJA? TAMUMVENI ZOMWE WAUZA ANTHU UKU.

Malawi Congress Party (MCP) Secretary General Richard Chimwendo Banda has said President Lazarus Chakwera is the only presidential candidate in the September 16 general elections who truly prioritizes the development of the nation. Speaking at a political rally held at Chatata Ground in Lilongwe City Central Constituency, Chimwendo Banda emphasized that President Chakwera has already…

Read More
People's party

KOMA AWAWA ANGANENE IZI KUCHIPINDA KWA MCP CHAKWERA AKUMVA?

Mwaimva? Akutitu wachiwiri kwa mtsogoleri wachipani cha Peoples PP, mchigawo chapakati, a Peter Kamange, auza anthu ku Mchinji kuti chipanichi motsogozedwa ndi mtsogoleri wake a Joyce Banda ndiwokonzeka kuthetsa mavuto azachuma omwe ali mdziko muno pano miyezi isanu ndi umodzi yokha atangotenga boma. A Kamange , anena izi pamsonkhano omwe anachititsa pa bwalo la Magawa….

Read More

KUTUKWANISA CHAKWERA OSALAKWA UKU ~ MBAVA ZA AZIMAYI AZIPANGA IZI KU LILONGWE KWA MCP

MWAIMVA? Akutitu apolisi ku Lilongwe amanga amayi atatu omwe akuwaganizira kuti mothandizidwa ndi anthu ena anathyola mnyumba ndikubamo katundu monga deep freezer, upright fridge, mattress, microwave ndi katundu wina. Amayiwa, malinga ndi mneneri wa polisi a Hastings Chigalu ndi a Chimwemwe Chembe a zaka 39, a Elizabeth Mkwezalamba a zaka 36 komanso a Memory Elias…

Read More

PHONE YA IPHONE IKWELASO MTENGO OSAFUNA ASIYE

Kodi inu amene mumafuna mutagula Iphone kapena muli nayo kale mukufuna mupange upgrade, Mwaimva iyi? Akuti anthu ogwiritsa ntchito lamya za IPhone atha kumazigula pa mtengo okwera ngati mtsogoleri wa dziko la America, a Donald Trump, apitilire ndi ganizo lake loyika msonkho wa 25 percent pa lamyazi zomwe imapanga ndi kampani ya Apple. A Trump…

Read More

KUZIZILA UKU ANA AGONE KU POLICE ZOONA?

Four (4) students were recently arrested at Mikundi School in Mchinji for exchanging answers during an examination. According to Dorothy Nampota, Executive Director of the Malawi National Examinations Board (MANEB), the students were caught swapping papers while the exams were ongoing. She added that despite this incident, the examinations are generally progressing well, with 257,129…

Read More

KOMA ABALE MUNTHU KUMUTELE ZOONA?

Kodi apapa nde tinene kuti kwayambika zotani nanga? Akuti apolisi m’boma la Mulanje akusakasaka anthu omwe apha ndikuotcha a Luka Saluwa a zaka 35 kaamba koti amawaganizira kuti anapha mayi Rita Maluku a zaka 43 ochokera kwa Misomali Kwa mfumu yaikulu Chikumbu m’boma la Mulanje. M’neneri wapolisi ya m’bomali a Innocent Moses ati lachitatu sabata…

Read More