...
MWAZIZIWA? > ZA BUSINESS
THUGS

LA 40 LAKWANA – AMAPHA ANTHU USIKU AJA AWAGWIRA.

Mwaziziwa? Zachitika lero ku Lilongwe, akuti Apolisi amanga anthu 108 omwe akuwaganizira kuti akhala akubera anthu komanso kupha, ku Kanengo ndi madera ena ozungulira. Wachiwiri kwa mneneri wa polisi ku Central West Region a Foster Benjamin wati anthuwa amangidwa mosiyanasiyana pa ntchito yomwe apolisi akhala akugwira masiku apitawa kutsatira ma lipoti a umbanda komanso kuphedwa…

Read More
Joe Kellz – Only You ft Phyzix x Lawrence Mbenjere

Joe Kellz – ”ONLY YOU” ft Phyzix x Lawrence Mbenjere

Joe Kellz features Phyzix and Lawrence Mbenjere in his latest release ONLY YOU. Kwanthawi yoyamba woyimba Joe Kellz wayimba limodzi nyimbo ndi Phyzix komanso Lawrence Mbenjere yomwe akuyitcha Only You. Nyimboyi yomwe yanyamula uthenga wokhudza za chikondi yajambulidwa ndi Malonie komanso Princox. Kanema wanyimboyi yemwe waikidwa kale pa tsamba la intaneti, wajambulidwa ndi Mega komanso…

Read More
Woman-charged-with-manslaughter-in-fatal-jet-ski-collision

NKHANI YOKUPHA MWANA NDI KUTHAWA

Mtsikana wachichepele dzina lake Ava Moore, yemwe anali ndi zaka 18 zokha, anamwalira atagundidwa ndi jet ski pamene anali kosangalala m’nyanja. Izi zinachitika kumapeto kwa sabata m’nyanja imene ili ku Texas. Mayi wina wazaka 21, dzina lake Daikerlyn Gonzalez, ndiye amene anali kuyendetsa jet ski. Uyu ndi wochokera ku Venezuela ndipo analowa m’dziko popanda zikalata…

Read More

WHY? Illovo Sugar Malawi Has partnered with the Ministry of Trade.

Illovo Sugar Malawi has reaffirmed its commitment to ensuring the availability of sugar on the local market by partnering with the Ministry of Trade and national security agencies to curb illegal sugar exports to neighbouring countries. This initiative aims to protect domestic consumers from artificial shortages and price instability. Acting Managing Director Kondwani Msimuko disclosed…

Read More
Mzimba

MZIMBA NAYO YATI CHUMA CHATHU OSACHITA NACHO ZOPUSA

Mwaziva? Mzimba si ya anthu ogona ayi. Akana zokuti ndalama za CDF azisunga ndi anduna. Nkhani ikuti, Citizens and civil society groups in Mzimba have welcomed the recent constitutional court decision that strips Members of Parliament (MPs) of direct control over the Constituency Development Fund (CDF). The ruling is being praised as a progressive move…

Read More

ANTHU ANDEVU ZAWO KUMAPANGA IZI ZOONA?

Nde mwaimva ya lero? akutitu apolisi ku Salima amanga abambo atatu kaamba kopezeka ndi migolo khumi ndi inayi ya mafuta a petulo okwana malita 200 uliwonse. Woyankhulira polisi ya m’bomali a Rabecca Ndiwate atsimikiza za izi ponena kuti anthu atatuwa ndi a Fatsan Phiri,Madalitso Dzindiwo komanso a Amidu Sipolo ndipo agwidwa loweluka ku Sengabay apolisi…

Read More

PHONE YA IPHONE IKWELASO MTENGO OSAFUNA ASIYE

Kodi inu amene mumafuna mutagula Iphone kapena muli nayo kale mukufuna mupange upgrade, Mwaimva iyi? Akuti anthu ogwiritsa ntchito lamya za IPhone atha kumazigula pa mtengo okwera ngati mtsogoleri wa dziko la America, a Donald Trump, apitilire ndi ganizo lake loyika msonkho wa 25 percent pa lamyazi zomwe imapanga ndi kampani ya Apple. A Trump…

Read More
Seraphinite AcceleratorOptimized by Seraphinite Accelerator
Turns on site high speed to be attractive for people and search engines.