...
MWAZIZIWA? > ENTERTAINMENT
Joe Kellz – Only You ft Phyzix x Lawrence Mbenjere

Joe Kellz – ”ONLY YOU” ft Phyzix x Lawrence Mbenjere

Joe Kellz features Phyzix and Lawrence Mbenjere in his latest release ONLY YOU. Kwanthawi yoyamba woyimba Joe Kellz wayimba limodzi nyimbo ndi Phyzix komanso Lawrence Mbenjere yomwe akuyitcha Only You. Nyimboyi yomwe yanyamula uthenga wokhudza za chikondi yajambulidwa ndi Malonie komanso Princox. Kanema wanyimboyi yemwe waikidwa kale pa tsamba la intaneti, wajambulidwa ndi Mega komanso…

Read More
MISS MALAWI 2025

BEAUTY CONTEST – MA MISS MALAWI A ULENDO UNO AKONGOLA ZA MWANO

Asungwana okwana khumi ndi anayi ndi omwe akhale akukathambitsana mu mpikisano wa chaka chino wa ziphadzuwa zolimbikitsa chikhalidwe wa Miss Culture Malawi. Mokonzedwa ndi a Lush Africa Foundation, mpikisanowu uchitika pa 29 November ku BICC mu mzinda wa Lilongwe. Asungwanawa ndi Leonorah Cooke, Lutondwa Mwenifumbo, Michelle Mwanamai, Natasha Kwaela, Mtendele Chimango, Mellisah Kamangira, Thokozani Lupoka,…

Read More
Theresa phodo ndi Praise Umali

PALIBE CHINSISI ZAZIWIKA LERO ZA ANTHU AWA

Iyi si miseche koma chilungamo cha nkhani. Praise Umali ndi Mkazi uyu Thereza Phodo abwela poyela sanafune abise mpaka kale. Monga mukudziwa za woyimba awa samadziwika mmene ankalowa mu gulu la Zathu ndi anzawo ena anayi. Koma adachilimika mpaka kuzama mu zisudzo komanso maimbidwe kufikira pomwe gulu la Zathu linazilala.Pano aluso wonse asanu ndi mmodzi…

Read More

ELI NJUCHI WAULURA UFITI WAKE OPEKA NYIMBO

Mutha kudabwa kuti bwanji tikuti ufiti, Ayi ndithu mwana uyu si mfiti koma kuti luso lake ndi loopsa kwambiri. Woyimba Uyu Eli Njuchi wati nyimbo zake amalemba komanso kupeka yekha ngakhale ena mpaka lero amamukayikira. Eli Njuchi yemwe chaka chino wakwanitsa zaka 24, wati kupatula kuyimba, luso lina lomwe Mulungu anamudalitsa nalo ndilolemba komanso kupeka….

Read More
Seraphinite AcceleratorOptimized by Seraphinite Accelerator
Turns on site high speed to be attractive for people and search engines.