BAE KUGULA ICHI MUKANILE CHIMUPHE YEKHA IWE MOYO WAKO UKHALEBE

Osazanena kuti ochenjeza panalibe. Mumve izi, akuti kafukufuku ku Canada wapeza umboni wamphamvu wosonyeza kuti kudya zakudya zambiri zokonzedwanso kwambiri kapena kuti over processed, monga zokhwasula-khwasula, zakudya zozizira, ndi chakudya cham’mawa maka zotsekemela za mgulu la ma cereals – kungayambitse matenda aakulu. Zakudya izi zili paliponse chifukwa ndizosavuta, zokoma, komanso zogulitsidwa kwambiri. Koma ofufuza akuti…

Read More

TRUMP WHY TRUMP? Trump Administration Suspends Student Visa Interviews Amid Intensified Surveillance Push

In a move that could profoundly disrupt academic mobility and financial stability for U.S. universities, the Trump administration has abruptly ordered U.S. embassies around the world to stop scheduling visa interviews for foreign students. This directive, buried in a State Department cable dated Tuesday, raises a pressing question: Why is a government so vocal about…

Read More
MALAWI POLICE

ANTHU AKAKWIYA SAONASO KUTI UYU NDI NDI PRESIDENT WATHU, KAYA NDI BWANA

Mwaimva? nkhani yomwe ili apa ndi yoopsa kwambiri imene ngakhale apolice sakumvesa kuti amalawi akakwiya angafike apa. Akutitu Apolisi m’boma la Ntchisi anjata anyamata 12 omwe amagwira ntchito ku kampani ya Malawi Electricity Access Project (MEAP) kaamba koti anamangilira akuluakulu awiri akampaniyi kumitengo pomwe amafuna kukakamiza akuluakulu akampaniyi kuti awapatse malipiro awo. Mneneri wa polisi…

Read More
Thabo Chakaka Nyirenda

KWAYAMBIKA NKHONDO YOMENYELANA MISONKHO YATHU KU BOMA

Mwaziziwa? Ndalama zathu amalawi zikufunika kuzisalira kudya zinthu sizili bwino. Nanga tangoganizani , akuti mlangizi wa boma pa za malamulo a Thabo Chakaka Nyirenda ati atengera chigamulo cha bwalo la zamalamulo (Constitutional Court) chokhudza kagwiritsidwe ntchito ka ndalama za chitukuko za CDF ku Bwalo lalikulu la Supreme. A Nyirenda awuza Times kuti apita ku bwaloli…

Read More

ANA ASUKULU ACHOSA KALE MIMBA 350 MIYEZI YOKHAYI KU MACHINGA?

Kodi awa sangadikile alowe kaye m’banja? Imagine akuti Machinga District has recorded over 350 cases of unsafe abortions between January and April this year, with the youngest case involving a 15-year-old girl. This alarming statistic was revealed by Jacqueline Kaminyu, Post-Abortion Care Coordinator at Machinga District Hospital, during a Multistakeholder Movement on Women and Girls…

Read More
SMARTMATIC

ANTHU OLIMBA MTIMA AKUFUNA KUTHANA NDI SMARTMATIC? ALIMBA?

The secretaries of the six political parties competing in the September 16 elections have reiterated their commitment to ending political violence, but have failed to take responsibility for their parties’ involvement in the matter. In a statement read to journalists at the Centre for Multiparty Democracy in Lilongwe, the secretaries said they were disappointed by…

Read More

Hiking for Hype? Scrutinizing MAGLA’s Environmental Commitment

The Malawi Gaming and Lotteries Authority (MAGLA)’s K5 million donation to the Public Relations Society of Malawi (PRSM) for the Zomba Mountain Fun Walk and Hike appears, on the surface, to be a gesture of environmental concern. However, the extent to which such financial contributions translate into meaningful environmental impact remains debatable. While MAGLA’s Public…

Read More

ANTHU ANDEVU ZAWO KUMAPANGA IZI ZOONA?

Nde mwaimva ya lero? akutitu apolisi ku Salima amanga abambo atatu kaamba kopezeka ndi migolo khumi ndi inayi ya mafuta a petulo okwana malita 200 uliwonse. Woyankhulira polisi ya m’bomali a Rabecca Ndiwate atsimikiza za izi ponena kuti anthu atatuwa ndi a Fatsan Phiri,Madalitso Dzindiwo komanso a Amidu Sipolo ndipo agwidwa loweluka ku Sengabay apolisi…

Read More