
MUNTHU WABELA MCHIMWENE WAKE KOMA MPAKA KUMUTELE ABALE?
Kodi abale nkhani iyi mukuyimva bwanji? akuti bwalo la Milandu m’boma la Mangochi lalamula Mayi wina wazaka 31 kuti akakhale kundende zaka zitatu atapezeka olakwa pa Mulandu wakuba katundu wa mchimwene wake wandalama zokwana K12 million. Oyimila Boma pa Mlanduwu Grace Mindozo anawuza bwalori kuti chaka chatha, mayi Cecelia Liotcha ankasunga katundu wa mchimwene wawo…