PALIBE CHINSISI ZAZIWIKA LERO ZA ANTHU AWA
Iyi si miseche koma chilungamo cha nkhani. Praise Umali ndi Mkazi uyu Thereza Phodo abwela poyela sanafune abise mpaka kale. Monga mukudziwa za woyimba awa samadziwika mmene ankalowa mu gulu la Zathu ndi anzawo ena anayi.
Koma adachilimika mpaka kuzama mu zisudzo komanso maimbidwe kufikira pomwe gulu la Zathu linazilala.Pano aluso wonse asanu ndi mmodzi akuchita zawo kumbali ya luso.
Theresa ndi Praise achita chamuna ndi maimbidwe kutulutsa nyimbo zambiri koma ulendo uno atulutsa nyimbo yotchedwa ‘Pray For Me.’
Ndi nyimboyi iwo akupereka uthenga wonena kuti tonse timaperewera pamaso pa Mulungu.
ENGLISH VERSION OF THIS
Singers Theresa Phondo and Praise Umali are not known for how they joined the group Zathu with four other members.
But they continued to delve into acting and singing until the group Zathu disappeared.
Now all six artists are doing their part in the field of art.
Theresa and Praise have been brave and musical to release many songs but this time they have released a song called ‘Pray For Me.’
With this song they are giving a message that we are all inadequate before God.
One thought on “PALIBE CHINSISI ZAZIWIKA LERO ZA ANTHU AWA”