KODI NDI ZA KUCHIPINDA ZOMWE UYU WAPHELA MKAZI WAKE?
Koma abale zina ukamva mmmh, Akuti Ku Chiradzulu apolisi amanga a Dyson Makawa powaganizila kuti apha mkazi wawo atasemphana pa nkhani zam’banja. Mneneri wa polisi m’bomali, a Cosmas Kagulo awuza Zodiak Online lero kuti a Makawa akuganiziridwa kuti anapha mkazi wawo Zione John yemwe anasiyana nayo atasemphana maganizo. Iwo ati pa 17 mwezi uno a…