KALINDO WAFIKA KALE KU MZUZU KOPANGA MA DEMO – APA ZAYIPA BASI
Mwaimva? akutitu yemwe ndi mtsogoleri wa gulu la Malawi First a Bon Kalindo wafika pabwalo lamasewelo la Katoto pomwe akhale akuchita nawo ziwonetselo zomwe zakonzedwa. A Kalindo ati iwo ndi m’malawi ndipo ziwonetselozi akupangitsanso ndi a Malawi ndichifukwa chake aganiza zopanga nawo ziwonetselozi Ku Mzuzu. Iwo ati siokondwa ndi kukwela Kwa mitengo ya zinthu komanso…