KODI IYISO NDE KAMPENI YANJI YOMWE SYMON KENDAL WAPANGAYI?
Oyimba wodziwika bwino m’dziko lino a Kendall Kamwendo yemwenso akufuna kudzapikisana nawo pa chisankho cha 16 September pa mpando wa phungu wa dera la Dowa Mndolera ngati phungu woyima payekha m’boma la Dowa lero wapereka Ambulance yoti izithandiza kutumikira anthu pa ntchito za umoyo kudelari. A Kamwendo ati agula ambulance yi ndi ndalama zawo kaamba…