ANTHU AKAKWIYA SAONASO KUTI UYU NDI NDI PRESIDENT WATHU, KAYA NDI BWANA
Mwaimva? nkhani yomwe ili apa ndi yoopsa kwambiri imene ngakhale apolice sakumvesa kuti amalawi akakwiya angafike apa. Akutitu Apolisi m’boma la Ntchisi anjata anyamata 12 omwe amagwira ntchito ku kampani ya Malawi Electricity Access Project (MEAP) kaamba koti anamangilira akuluakulu awiri akampaniyi kumitengo pomwe amafuna kukakamiza akuluakulu akampaniyi kuti awapatse malipiro awo. Mneneri wa polisi…